Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 9:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako anatumiza makalata a mawu amtendere ndi odalirika+ kwa Ayuda onse m’zigawo 127+ zimene Ahasiwero+ anali kulamulira.

  • Salimo 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+

      Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+

      ו [Waw]

      Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+

  • Salimo 38:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Palibe pabwino m’thupi langa chifukwa cha chidzudzulo chanu.+

      Ndipo m’mafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+

  • Salimo 43:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+

      Zimenezi zinditsogolere.+

      Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+

  • Salimo 86:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+

      Ndidzayenda m’choonadi chanu.+

      Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+

  • Yesaya 38:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye anapemphera kuti: “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena