Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno ndinauza Alevi+ kuti pobwera azidziyeretsa nthawi zonse+ komanso azilondera zipata za mzinda+ kuti tsiku la sabata likhale loyera.+ Inu Mulungu wanga, mundikumbukirenso+ pa zimenezi ndipo mundimvere chifundo malinga ndi kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+

  • Salimo 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.+

      Alandire mafuta a nsembe zanu zopsereza.+ [Seʹlah.]

  • 1 Akorinto 15:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba,+ osasunthika, okhala ndi zochita zambiri nthawi zonse mu ntchito ya Ambuye,+ podziwa kuti zonse zimene mukuchita mu ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+

  • Aheberi 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena