Nehemiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino+ zonse zimene ndachitira anthu awa.+ Nehemiya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko. Nehemiya 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ngakhale ntchito yobweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndi mbewu zoyamba kucha. Inu Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino zimene ndinachita.+
14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko.
31 ngakhale ntchito yobweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndi mbewu zoyamba kucha. Inu Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino zimene ndinachita.+