Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mundikumbukire,+ inu Mulungu wanga, chifukwa cha zinthu zimenezi ndipo musaiwale+ ntchito za kukoma mtima kosatha zimene ndachitira nyumba+ ya Mulungu wanga ndi onse otumikira kumeneko.

  • Nehemiya 13:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 ngakhale ntchito yobweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndi mbewu zoyamba kucha.

      Inu Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino zimene ndinachita.+

  • Salimo 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+

      Andibwezere mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga pamaso pake.+

  • Salimo 106:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndikumbukireni inu Yehova, ndipo ndisonyezeni kukoma mtima kumene mumasonyeza anthu anu.+

      Ndisamalireni ndi kundipulumutsa,+

  • Malaki 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova+ analankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu ndi kumvetsera.+ Buku la chikumbutso linayamba kulembedwa pamaso pake.+ Buku limeneli linali lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene anali kuganizira za dzina lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena