Mateyu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba. Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba.
10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.