Mateyu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro, pita kagulitse katundu wako ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+ Maliko 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu anamuyang’ana ndipo anam’konda. Kenako anamuuza kuti: “Chinthu chimodzi chikusowekabe mwa iwe: Pita kagulitse zilizonse zimene uli nazo ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba, ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+ Luka 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge. Luka 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atamva zimenezo, Yesu anamuuza kuti: “Pali chinthu chimodzi chimene chikusowekabe mwa iwe: Kagulitse zinthu zonse zimene uli nazo n’kugawa ndalamazo kwa anthu osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba, ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+
21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro, pita kagulitse katundu wako ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+
21 Yesu anamuyang’ana ndipo anam’konda. Kenako anamuuza kuti: “Chinthu chimodzi chikusowekabe mwa iwe: Pita kagulitse zilizonse zimene uli nazo ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba, ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+
33 Gulitsani+ zinthu zanu ndi kupereka mphatso zachifundo.+ Dzipangireni zikwama za ndalama zomwe sizingathe, kutanthauza chuma chosatha kumwamba,+ kumene mbala singafikeko, ndipo njenjete* singawononge.
22 Atamva zimenezo, Yesu anamuuza kuti: “Pali chinthu chimodzi chimene chikusowekabe mwa iwe: Kagulitse zinthu zonse zimene uli nazo n’kugawa ndalamazo kwa anthu osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba, ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+