Mateyu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba. 1 Timoteyo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndiponso asunge+ maziko abwino+ a tsogolo lawo monga chuma, kuti agwire mwamphamvu moyo weniweniwo.+
20 Koma unjikani chuma chanu kumwamba,+ kumene njenjete kapena dzimbiri sizingawononge,+ ndiponso kumene mbala sizingathyole n’kuba.
19 ndiponso asunge+ maziko abwino+ a tsogolo lawo monga chuma, kuti agwire mwamphamvu moyo weniweniwo.+