Luka 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera. Luka 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+
41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera.
9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+