Mateyu 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+ Yohane 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’nyumba ya Atate wanga muli malo ambiri okhalamo.+ Akanapanda kukhalamo, ndikanakuuzani, chifukwa ndikupita kukakukonzerani malo.+
34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+
2 M’nyumba ya Atate wanga muli malo ambiri okhalamo.+ Akanapanda kukhalamo, ndikanakuuzani, chifukwa ndikupita kukakukonzerani malo.+