Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 kuti zikwaniritsidwe zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri amene anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mafanizo, ndidzafalitsa zinthu zobisika kuchokera pa chiyambi cha dziko lapansi.”+

  • Aheberi 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Zikanatero, akanavutika mobwerezabwereza kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.+ Koma tsopano iye waonekera+ kamodzi+ kokha pa mapeto a nthawi* zino+ kuti achotse uchimo kudzera mu nsembe yake.+

  • 1 Petulo 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye anadziwikiratu dziko lisanakhazikitsidwe,+ koma anaonekera pa nthawi ya mapeto chifukwa cha inuyo,+

  • Chivumbulutso 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo onse okhala padziko lapansi adzachilambira. Anthu onsewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu+ wa moyo, umene Mwanawankhosa amene anaphedwa,+ ndiye mwiniwake. Mpukutuwo unakonzedwa kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena