Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+ 1 Petulo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anadziwikiratu dziko lisanakhazikitsidwe,+ koma anaonekera pa nthawi ya mapeto chifukwa cha inuyo,+
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
20 Iye anadziwikiratu dziko lisanakhazikitsidwe,+ koma anaonekera pa nthawi ya mapeto chifukwa cha inuyo,+