Akolose 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake. Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.
26 Mawuwo ndi chinsinsi chopatulika+ chimene chinabisidwa nthawi* zakale,+ ndiponso kwa mibadwo yakale. Koma tsopano chaululidwa+ kwa oyera ake.
3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.