1 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.
4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.