1 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Mulungu wavomereza kuti tipatsidwe ntchito yolalikira uthenga wabwino. Choncho sitikulankhula nʼcholinga chosangalatsa anthu, koma Mulungu amene amafufuza mitima yathu.+ 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, ptsa. 30-31
4 Koma Mulungu wavomereza kuti tipatsidwe ntchito yolalikira uthenga wabwino. Choncho sitikulankhula nʼcholinga chosangalatsa anthu, koma Mulungu amene amafufuza mitima yathu.+