Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+ Yohane 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo Yesu anati: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ pakuti ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano.+ Sindinabwere mwakufuna kwanga ayi, koma Iyeyo anandituma.+
17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+
42 Pamenepo Yesu anati: “Mulungu akanakhala Atate wanu, mukanandikonda,+ pakuti ine ndinachokera kwa Mulungu ndipo ndili pano.+ Sindinabwere mwakufuna kwanga ayi, koma Iyeyo anandituma.+