Yohane 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti Atateyo amakukondani, chifukwa munandikonda+ ine ndipo mwakhulupirira kuti ine ndinabwera monga nthumwi ya Atate.+ 1 Yohane 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+
27 Pakuti Atateyo amakukondani, chifukwa munandikonda+ ine ndipo mwakhulupirira kuti ine ndinabwera monga nthumwi ya Atate.+
5 Onse amene amakhulupirira kuti Yesu ndi Khristu, ndi ana a Mulungu,+ ndipo onse amene amakonda Atate amakondanso mwana wake.+