Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+

  • Yohane 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Poyankha Yesu anati:+ “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kuona ufumu wa Mulungu atapanda kubadwanso.”+

  • 1 Petulo 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+

  • 1 Yohane 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Aliyense amene ali mwana wa Mulungu sapitiriza kuchita tchimo,+ chifukwa mbewu ya Mulungu yopatsa moyo imakhalabe mwa munthu ameneyo, ndipo sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, chifukwa ndi mwana wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena