Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+ Yohane 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 chifukwa mawu amene munandipatsa ndawapereka kwa iwo.+ Iwo awalandira ndipo adziwa ndithu kuti ine ndinabwera monga nthumwi yanu,+ ndipo akhulupirira kuti ndinu amene munandituma.+
13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+
8 chifukwa mawu amene munandipatsa ndawapereka kwa iwo.+ Iwo awalandira ndipo adziwa ndithu kuti ine ndinabwera monga nthumwi yanu,+ ndipo akhulupirira kuti ndinu amene munandituma.+