Yohane 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti Atateyo amakukondani, chifukwa munandikonda+ ine ndipo mwakhulupirira kuti ine ndinabwera monga nthumwi ya Atate.+ Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
27 Pakuti Atateyo amakukondani, chifukwa munandikonda+ ine ndipo mwakhulupirira kuti ine ndinabwera monga nthumwi ya Atate.+
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+