Aheberi 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+ Aheberi 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero, ndiye chifukwa chake iye ali mkhalapakati+ wa pangano latsopano kuti anthu amene aitanidwa alandire lonjezo la cholowa chamuyaya.+ Izi zatheka chifukwa cha imfa yake, imene inali ngati dipo+ lawo lowamasula ku machimo amene iwo anali nawo m’pangano lakale lija.+
8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+
15 Chotero, ndiye chifukwa chake iye ali mkhalapakati+ wa pangano latsopano kuti anthu amene aitanidwa alandire lonjezo la cholowa chamuyaya.+ Izi zatheka chifukwa cha imfa yake, imene inali ngati dipo+ lawo lowamasula ku machimo amene iwo anali nawo m’pangano lakale lija.+