Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Aheberi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye amasonyeza ndendende mmene ulemerero wa Mulungu ulili+ ndipo ndiye chithunzi chenicheni cha Mulungu weniweniyo,+ ndipo amachirikiza zinthu zonse mwa mawu ake amphamvu.+ Atatiyeretsa potichotsera machimo athu,+ anakhala pansi kudzanja lamanja+ la Wolemekezeka m’malo okwezeka.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
3 Iye amasonyeza ndendende mmene ulemerero wa Mulungu ulili+ ndipo ndiye chithunzi chenicheni cha Mulungu weniweniyo,+ ndipo amachirikiza zinthu zonse mwa mawu ake amphamvu.+ Atatiyeretsa potichotsera machimo athu,+ anakhala pansi kudzanja lamanja+ la Wolemekezeka m’malo okwezeka.+