Yohane 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Mulungu anatumiza Mwana wake m’dziko, osati kuti mwanayo adzaweruze+ dziko, koma kuti mwa iye, dziko lipulumutsidwe.+ Yohane 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ine ndikumudziwa,+ chifukwa ndine nthumwi. Iyeyu anandituma ine.”+
17 Pakuti Mulungu anatumiza Mwana wake m’dziko, osati kuti mwanayo adzaweruze+ dziko, koma kuti mwa iye, dziko lipulumutsidwe.+