Luka 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mwana wa munthu anabwera kudzafunafuna ndi kupulumutsa anthu osochera.”+ 1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo. 1 Timoteyo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mawu akuti Khristu Yesu anabwera m’dziko kudzapulumutsa ochimwa,+ ndi mawu oona ndi oyenera kuwavomereza ndi mtima wonse.+ Mwa ochimwa amenewa, ine ndiye wochimwa kwambiri.+ 1 Yohane 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+ 1 Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso ife taona+ ndipo tikuchitira umboni+ kuti Atate anatumiza Mwana wake kuti akhale Mpulumutsi wa dziko.+
15 Mawu akuti Khristu Yesu anabwera m’dziko kudzapulumutsa ochimwa,+ ndi mawu oona ndi oyenera kuwavomereza ndi mtima wonse.+ Mwa ochimwa amenewa, ine ndiye wochimwa kwambiri.+
14 Komanso ife taona+ ndipo tikuchitira umboni+ kuti Atate anatumiza Mwana wake kuti akhale Mpulumutsi wa dziko.+