Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+

  • Yohane 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti Mulungu anatumiza Mwana wake m’dziko, osati kuti mwanayo adzaweruze+ dziko, koma kuti mwa iye, dziko lipulumutsidwe.+

  • Yohane 4:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Iwo anayamba kuuza mayi uja kuti: “Sikuti tikukhulupirira chifukwa cha mawu ako ajanso ayi, pakuti tadzimvera tokha+ ndipo tadziwa ndithu kuti munthu uyu ndi mpulumutsi+ wa dziko.”

  • Yohane 12:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Ngati munthu wamva mawu anga koma osawasunga, ine sindiweruza woteroyo, pakuti sindinabwere kudzaweruza dziko,+ koma kudzalipulumutsa.+

  • Machitidwe 5:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena