Machitidwe 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+
31 Ameneyo Mulungu anamukweza kudzanja lake lamanja+ monga Mtumiki Wamkulu+ ndi Mpulumutsi.+ Anachita zimenezi kuti Aisiraeli alape+ ndi kuti machimo awo akhululukidwe.+