Mateyu 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma sanagone+ naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamutcha dzina lakuti Yesu.+ Luka 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano mvetsera! Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna.+ Udzam’patse dzina lakuti Yesu.+ Luka 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+
31 Tsopano mvetsera! Udzakhala ndi pakati ndipo udzabereka mwana wamwamuna.+ Udzam’patse dzina lakuti Yesu.+
21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+