Mateyu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+ Luka 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+
21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+
21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+