Genesis 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mngelo wa Yehovayo anapitiriza kulankhula ndi mkaziyo kuti: “Taona, panopo uli ndi pakati, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamutche Isimaeli,+ pakuti Yehova wamva kulira kwako.+ Oweruza 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo+ ndi kumuuza kuti: “Tamvera, panopa ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna.+ Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+
11 Mngelo wa Yehovayo anapitiriza kulankhula ndi mkaziyo kuti: “Taona, panopo uli ndi pakati, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamutche Isimaeli,+ pakuti Yehova wamva kulira kwako.+
3 Ndiyeno tsiku lina, mngelo wa Yehova anaonekera kwa mkaziyo+ ndi kumuuza kuti: “Tamvera, panopa ndiwe wosabereka ndipo ulibe mwana. Koma udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna.+
4 Koma nthawi itakwana,+ Mulungu anatumiza Mwana wake,+ amene anadzabadwa kwa mkazi+ ndipo anadzakhala pansi pa chilamulo.+