Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Kenako azipha mbuzi ya nsembe yamachimo yoperekera anthuwo,+ n’kulowa ndi magazi ake kuchipinda, kuseri kwa nsalu yotchinga.+ Kumeneko magaziwo+ azichita nawo zimene anachita ndi magazi a ng’ombe yamphongo ija. Azidontheza magaziwo patsogolo pa chivundikiro.

  • Mateyu 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mofanana ndi zimenezi, Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa, koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuwombola anthu ambiri.”+

  • Yohane 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+

  • Yohane 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Ndili ndi nkhosa zina+ zimene sizili za khola ili,+ zimenezonso ndiyenera kuzibweretsa. Zidzamva mawu anga,+ ndipo zidzakhala gulu limodzi ndi m’busa mmodzi.+

  • Chivumbulutso 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nthawi yomweyo, ndinamuyankha kuti: “Mbuyanga, mukudziwa ndinu.” Ndipo iye anati: “Amenewa ndi amene atuluka m’chisautso chachikulu,+ ndipo achapa mikanjo yawo ndi kuiyeretsa+ m’magazi+ a Mwanawankhosa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena