Luka 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa kuti alape.”+ 2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+ 1 Yohane 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+