Salimo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.+ Chivumbulutso 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+
3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+