Aroma 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza pamene tinali ofooka,+ Khristu anafera anthu osapembedza Mulungu pa nthawi yoikidwiratu.+ Aroma 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ngati dziko layanjidwa ndi Mulungu chifukwa chakuti iwo anatayidwa,+ ndiye kuti akadzalandiridwa+ zidzatanthauza moyo kuchokera ku imfa. 1 Yohane 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+
15 Chifukwa ngati dziko layanjidwa ndi Mulungu chifukwa chakuti iwo anatayidwa,+ ndiye kuti akadzalandiridwa+ zidzatanthauza moyo kuchokera ku imfa.