Mateyu 21:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ichi n’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu n’kuperekedwa kwa mtundu wobala zipatso zake.+ Aheberi 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wapanga loyambalo kukhala lotha ntchito.+ Tsopano pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, latsala pang’ono kufafanizika.+
43 Ichi n’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu n’kuperekedwa kwa mtundu wobala zipatso zake.+
13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wapanga loyambalo kukhala lotha ntchito.+ Tsopano pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, latsala pang’ono kufafanizika.+