Aroma 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Khristu ndiye kutha kwa Chilamulo,+ kuti aliyense wokhulupirira akhale wolungama.+ Aheberi 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano popeza kuti unsembewo ukusinthidwa,+ ndiye kuti chilamulonso chifunika kusintha.+