Aroma 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+ 2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+
11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+