Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina. 2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina.
17 Pakuti iye analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu Atate,+ pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu, kuti: “Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye.”+