Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+ Luka 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba, akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+
5 Mawu ake adakali m’kamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba, ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa, amene ndikukondwera naye,+ muzimumvera.”+
22 Pamenepo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba, akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+