Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+ Luka 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+
35 Ndiyeno mawu+ anatuluka mumtambomo akuti: “Uyu ndiye Mwana wanga, amene ndinam’sankha.+ Mumvereni.”+