2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+ Aroma 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 koma amene Mulungu mwa mphamvu+ yake anam’lengeza kukhala Mwana wake+ mwa mzimu woyera+ pomuukitsa kwa akufa.+ Ameneyu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu. Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+ Aheberi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ mwa kudziika yekha kukhala mkulu wa ansembe.+ Koma amene anamupatsa+ ulemerero umenewo ndi amene analankhula zokhudza iyeyu kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako.”+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
17 Panamvekanso mawu+ ochokera kumwamba onena kuti: “Uyu ndiye Mwana wanga+ wokondedwa,+ amene ndimakondwera naye.”+
4 koma amene Mulungu mwa mphamvu+ yake anam’lengeza kukhala Mwana wake+ mwa mzimu woyera+ pomuukitsa kwa akufa.+ Ameneyu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu.
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ mwa kudziika yekha kukhala mkulu wa ansembe.+ Koma amene anamupatsa+ ulemerero umenewo ndi amene analankhula zokhudza iyeyu kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako.”+