Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Machitidwe 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa lonjezo lonselo kwa ife ana awo mwa kuukitsa Yesu.+ Zimenezi n’zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala Atate wako.’+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa lonjezo lonselo kwa ife ana awo mwa kuukitsa Yesu.+ Zimenezi n’zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala Atate wako.’+