Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+ Aheberi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ mwa kudziika yekha kukhala mkulu wa ansembe.+ Koma amene anamupatsa+ ulemerero umenewo ndi amene analankhula zokhudza iyeyu kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako.”+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ mwa kudziika yekha kukhala mkulu wa ansembe.+ Koma amene anamupatsa+ ulemerero umenewo ndi amene analankhula zokhudza iyeyu kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako.”+