1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna. Chivumbulutso 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo munawasandutsa mafumu+ ndi ansembe+ a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.”
12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.
10 Ndipo munawasandutsa mafumu+ ndi ansembe+ a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.”