Agalatiya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+ Aefeso 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero ine, amene ndili m’ndende+ chifukwa cha Ambuye, ndikukuchondererani kuti muziyenda moyenera+ kuitana kumene munaitanidwa nako.+ Akolose 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tikupemphereranso kuti muziyenda mogwirizana ndi zimene Yehova+ amafuna,+ kuti muzimukondweretsa pa chilichonse,+ pamene mukupitiriza kubala zipatso m’ntchito iliyonse yabwino, ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+ 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
16 M’malomwake ndikuti, Pitirizani kuyenda mwa mzimu,+ ndipo simudzatsatira chilakolako cha thupi ngakhale pang’ono.+
4 Chotero ine, amene ndili m’ndende+ chifukwa cha Ambuye, ndikukuchondererani kuti muziyenda moyenera+ kuitana kumene munaitanidwa nako.+
10 Tikupemphereranso kuti muziyenda mogwirizana ndi zimene Yehova+ amafuna,+ kuti muzimukondweretsa pa chilichonse,+ pamene mukupitiriza kubala zipatso m’ntchito iliyonse yabwino, ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+