Aefeso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru+ ndi kuti mumvetse zimene Iye akuulula mogwirizana ndi kumudziwa molondola.+ 2 Petulo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna kuti mulandire kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wowonjezereka.+ Kuti muchite zimenezi, mumudziwe molondola+ Mulungu ndi Yesu Ambuye wathu. 2 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati zinthu zimenezi zili mwa inu ndipo zikusefukira, zidzakutetezani kuti musakhale ozilala kapena osabala zipatso+ pa zimene mukuchita mogwirizana ndi kumudziwa molondola Ambuye wathu Yesu Khristu.
17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru+ ndi kuti mumvetse zimene Iye akuulula mogwirizana ndi kumudziwa molondola.+
2 Ndikufuna kuti mulandire kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wowonjezereka.+ Kuti muchite zimenezi, mumudziwe molondola+ Mulungu ndi Yesu Ambuye wathu.
8 Ngati zinthu zimenezi zili mwa inu ndipo zikusefukira, zidzakutetezani kuti musakhale ozilala kapena osabala zipatso+ pa zimene mukuchita mogwirizana ndi kumudziwa molondola Ambuye wathu Yesu Khristu.