2 Petulo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu ndi mtendere wake ziwonjezereke kwa inu. Kuti zimenezi zitheke, muyenera kudziwa molondola+ Mulungu komanso Yesu Ambuye wathu. 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 104/15/1987, ptsa. 15-20
2 Kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu ndi mtendere wake ziwonjezereke kwa inu. Kuti zimenezi zitheke, muyenera kudziwa molondola+ Mulungu komanso Yesu Ambuye wathu.