Akolose 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+ 1 Timoteyo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene chifuniro chake n’chakuti anthu, kaya akhale a mtundu wotani,+ apulumuke+ ndi kukhala odziwa choonadi+ molondola.+
9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+
4 amene chifuniro chake n’chakuti anthu, kaya akhale a mtundu wotani,+ apulumuke+ ndi kukhala odziwa choonadi+ molondola.+