Yesaya 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tembenukirani kwa ine kuti mupulumuke,+ inu nonse amene muli kumapeto kwa dziko lapansi, pakuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina.+ Machitidwe 17:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+ 1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.
22 “Tembenukirani kwa ine kuti mupulumuke,+ inu nonse amene muli kumapeto kwa dziko lapansi, pakuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina.+
30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+
13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.