Aefeso 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 umene ndili kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo, ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima monga mmene ndiyenera kuchitira.+ Filimoni 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndikukupempha mwachikondi,+ poona mmene ndililimu. Ineyo Paulo ndine wachikulire, komanso tsopano ndine mkaidi+ chifukwa cha Khristu Yesu.
20 umene ndili kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo, ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima monga mmene ndiyenera kuchitira.+
9 ndikukupempha mwachikondi,+ poona mmene ndililimu. Ineyo Paulo ndine wachikulire, komanso tsopano ndine mkaidi+ chifukwa cha Khristu Yesu.