Aroma 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+
30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+