Aroma 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, mmene zinakhalira kuti mwa uchimo umodzi anthu kaya akhale amtundu wotani anaweruzidwa kukhala ochimwa,+ momwemonso mwa kuchita chinthu chimodzi cholungamitsa,+ anthu kaya akhale amtundu wotani+ akuyesedwa olungama kuti akhale ndi moyo.+ 1 Akorinto 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+ Tito 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti titayesedwa olungama+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tikhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+
18 Chotero, mmene zinakhalira kuti mwa uchimo umodzi anthu kaya akhale amtundu wotani anaweruzidwa kukhala ochimwa,+ momwemonso mwa kuchita chinthu chimodzi cholungamitsa,+ anthu kaya akhale amtundu wotani+ akuyesedwa olungama kuti akhale ndi moyo.+
11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+
7 kuti titayesedwa olungama+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tikhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+